Aefeso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 komanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, Khristu akhale m’mitima yanu, pamodzi ndi chikondi+ chimene chiyenera kukhala pakati panu, ndiponso kuti muzike mizu+ ndi kukhala okhazikika pamaziko.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,10/15/2009, tsa. 267/15/1999, tsa. 14
17 komanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, Khristu akhale m’mitima yanu, pamodzi ndi chikondi+ chimene chiyenera kukhala pakati panu, ndiponso kuti muzike mizu+ ndi kukhala okhazikika pamaziko.+