Aefeso 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, tsa. 22
6 Munthu asakupusitseni ndi mawu opanda pake,+ pakuti mkwiyo wa Mulungu udzafika pa ana a kusamvera, ochita zinthu zimene ndatchulazi.+