Afilipi 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngakhale kuti ndikudzipereka ngati nsembe yachakumwa imene ikuthiridwa+ pansembe+ ndi pa ntchito yotumikira anthu imene chikhulupiriro chakupatsani,+ ndine wokondwa ndipo ndikukondwera+ ndi inu nonse. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142 Nsanja ya Olonda,11/15/2000, tsa. 12
17 Ngakhale kuti ndikudzipereka ngati nsembe yachakumwa imene ikuthiridwa+ pansembe+ ndi pa ntchito yotumikira anthu imene chikhulupiriro chakupatsani,+ ndine wokondwa ndipo ndikukondwera+ ndi inu nonse.