Afilipi 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho, tiyeni tonse amene tili okhwima mwauzimu,+ tikhale ndi maganizo amenewa.+ Ndipo ngati muli ndi maganizo osiyana ndi amenewa m’mbali ina iliyonse, Mulungu adzakuululirani maganizo oyenerawo. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Nsanja ya Olonda,9/1/2000, ptsa. 8-9
15 Choncho, tiyeni tonse amene tili okhwima mwauzimu,+ tikhale ndi maganizo amenewa.+ Ndipo ngati muli ndi maganizo osiyana ndi amenewa m’mbali ina iliyonse, Mulungu adzakuululirani maganizo oyenerawo.