Akolose 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndikulembera oyera ndi abale okhulupirika amene ali ogwirizana+ ndi Khristu ku Kolose, kuti: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate wathu zikhale nanu.+
2 ndikulembera oyera ndi abale okhulupirika amene ali ogwirizana+ ndi Khristu ku Kolose, kuti: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate wathu zikhale nanu.+