Akolose 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinakhala mtumiki+ wa mpingo umenewu mogwirizana ndi udindo+ umene Mulungu anandipatsa, woti ndilalikire mawu a Mulungu mokwanira, kuti inuyo mupindule.
25 Ndinakhala mtumiki+ wa mpingo umenewu mogwirizana ndi udindo+ umene Mulungu anandipatsa, woti ndilalikire mawu a Mulungu mokwanira, kuti inuyo mupindule.