Akolose 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuna kuti mudziwe nkhondo+ yaikulu imene ndikumenya chifukwa cha inuyo ndi anthu a ku Laodikaya,+ ndi onse amene sanandionepo maso ndi maso. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,7/15/2009, ptsa. 3-4
2 Ndikufuna kuti mudziwe nkhondo+ yaikulu imene ndikumenya chifukwa cha inuyo ndi anthu a ku Laodikaya,+ ndi onse amene sanandionepo maso ndi maso.