1 Atesalonika 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anatifera,+ kuti kaya tikhala maso kapena tigona, tikhale ndi moyo limodzi ndi iye.+