2 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kuti onsewo adzaweruzidwe chifukwa sanakhulupirire choonadi,+ koma anakonda zosalungama.+