1 Timoteyo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu ena akana kutsatira zimenezi ndipo asocheretsedwa+ n’kuyamba kutsatira nkhani zopanda pake.+