1 Timoteyo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho, poyamba ndikuchonderera nonse kuti muzipereka mapembedzero kwa Mulungu, muzipereka mapemphero,+ muzipemphererana, ndipo muzipereka mapemphero oyamika Mulungu m’malo mwa anthu onse, kaya akhale a mtundu wotani.+ 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,5/1/1996, tsa. 20
2 Choncho, poyamba ndikuchonderera nonse kuti muzipereka mapembedzero kwa Mulungu, muzipereka mapemphero,+ muzipemphererana, ndipo muzipereka mapemphero oyamika Mulungu m’malo mwa anthu onse, kaya akhale a mtundu wotani.+