1 Timoteyo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna otumikira bwino amakhala ndi mbiri yabwino+ ndi ufulu waukulu wa kulankhula+ za chikhulupiriro, mwa Khristu Yesu. 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 55 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 29
13 Pakuti amuna otumikira bwino amakhala ndi mbiri yabwino+ ndi ufulu waukulu wa kulankhula+ za chikhulupiriro, mwa Khristu Yesu.