Aheberi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo Mose monga wantchito+ anali wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu. Utumiki wakewo unali umboni wa zinthu zimene zidzalankhulidwe m’tsogolo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 11
5 Ndipo Mose monga wantchito+ anali wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu. Utumiki wakewo unali umboni wa zinthu zimene zidzalankhulidwe m’tsogolo.+