Aheberi 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amakhala woleza mtima pochita zinthu ndi anthu osadziwa kanthu ndi olakwa, chifukwa iyenso ndi wofooka.+
2 Amakhala woleza mtima pochita zinthu ndi anthu osadziwa kanthu ndi olakwa, chifukwa iyenso ndi wofooka.+