Aheberi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwachitsanzo, nthaka imamwa madzi a mvula imene imagwera panthakapo kawirikawiri. Kenako imatulutsa zomera zimene zimapindulitsa amene ailima.+ Nthaka imeneyi imalandiranso dalitso kuchokera kwa Mulungu.
7 Mwachitsanzo, nthaka imamwa madzi a mvula imene imagwera panthakapo kawirikawiri. Kenako imatulutsa zomera zimene zimapindulitsa amene ailima.+ Nthaka imeneyi imalandiranso dalitso kuchokera kwa Mulungu.