Aheberi 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma munthu amene sanachokere mumzere wobadwira+ wa Levi analandira chakhumi kwa Abulahamu,+ ndipo anadalitsa munthu amene anali ndi malonjezo.+
6 Koma munthu amene sanachokere mumzere wobadwira+ wa Levi analandira chakhumi kwa Abulahamu,+ ndipo anadalitsa munthu amene anali ndi malonjezo.+