Aheberi 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Alevi anali kulandira zakhumi ndipo ndi anthu oti amafa. Koma munthu wina amene analandira zakhumi,+ Malemba amamuchitira umboni kuti ali moyo.+
8 Alevi anali kulandira zakhumi ndipo ndi anthu oti amafa. Koma munthu wina amene analandira zakhumi,+ Malemba amamuchitira umboni kuti ali moyo.+