Aheberi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti munthu amene akufotokozedwa ndi zinthu zimene zatchulidwazi ndi wa fuko lina,+ ndipo palibe aliyense wa fuko limenelo amene anatumikirapo paguwa lansembe.+
13 Pakuti munthu amene akufotokozedwa ndi zinthu zimene zatchulidwazi ndi wa fuko lina,+ ndipo palibe aliyense wa fuko limenelo amene anatumikirapo paguwa lansembe.+