Aheberi 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti mkulu wa ansembe aliyense amaikidwa kuti azipereka zonse ziwiri, mphatso ndi nsembe.+ Ndiye chifukwa chake kunali kofunika kuti uyunso akhale ndi chinachake chopereka.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2000, tsa. 14
3 Pakuti mkulu wa ansembe aliyense amaikidwa kuti azipereka zonse ziwiri, mphatso ndi nsembe.+ Ndiye chifukwa chake kunali kofunika kuti uyunso akhale ndi chinachake chopereka.+