Aheberi 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pangano loyamba lija likanakhala lopanda zolakwika, sipakanafunikanso pangano lachiwiri.+