Aheberi 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti iye akuimba anthu mlandu pamene akunena kuti: “‘Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ watero Yehova.+
8 Pakuti iye akuimba anthu mlandu pamene akunena kuti: “‘Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano ndi nyumba ya Isiraeli komanso ndi nyumba ya Yuda,’ watero Yehova.+