Aheberi 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Munthu sadzaphunzitsa nzika inzake kapena m’bale wake kuti: “Um’dziwe Yehova!”+ Pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa,+ kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu.
11 “‘Munthu sadzaphunzitsa nzika inzake kapena m’bale wake kuti: “Um’dziwe Yehova!”+ Pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa,+ kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu.