Aheberi 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano, pangano loyamba lija linali ndi malamulo ake a utumiki wopatulika+ ndiponso malo ake oyera a padziko lapansi.+
9 Tsopano, pangano loyamba lija linali ndi malamulo ake a utumiki wopatulika+ ndiponso malo ake oyera a padziko lapansi.+