Aheberi 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.
5 Koma pamwamba pa likasalo panali akerubi aulemerero+ amene zithunzithunzi zawo zinali kugwera pachivundikiro chophimba machimo.+ Koma ino si nthawi yofotokoza zinthu zimenezi mwatsatanetsatane.