Aheberi 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 28 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 161
19 Chotero abale, ndife olimba mtima chifukwa tikugwiritsa ntchito njira yolowera+ m’malo oyera+ kudzera m’magazi a Yesu.