29 Ndiye kuli bwanji munthu amene wapondaponda+ Mwana wa Mulungu, amene akuona magazi+ a pangano amene anayeretsedwa nawo ngati chinthu wamba, amenenso wanyoza mzimu+ wa Mulungu, yemwe amasonyeza kukoma mtima kwakukulu? Munthu ameneyu akuyenera kulandira chilango chachikulu kwambiri.+