Aheberi 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choteronso, kuchokera mwa mwamuna mmodzi,+ amene anali ngati wakufa,+ kunabadwa ana ochuluka ngati nyenyezi zakumwamba komanso osawerengeka ngati mchenga wa m’mbali mwa nyanja.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:12 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, tsa. 171/15/1987, tsa. 12
12 Choteronso, kuchokera mwa mwamuna mmodzi,+ amene anali ngati wakufa,+ kunabadwa ana ochuluka ngati nyenyezi zakumwamba komanso osawerengeka ngati mchenga wa m’mbali mwa nyanja.+