Aheberi 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mwa chikhulupiriro, pamene Abulahamu anayesedwa,+ zinali ngati wapereka kale Isaki nsembe. Choncho munthu ameneyu, amene analandira malonjezo mokondwera, anali wokonzeka kupereka nsembe mwana wake wobadwa yekha.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2017, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,8/15/1998, ptsa. 11-121/15/1987, tsa. 13
17 Mwa chikhulupiriro, pamene Abulahamu anayesedwa,+ zinali ngati wapereka kale Isaki nsembe. Choncho munthu ameneyu, amene analandira malonjezo mokondwera, anali wokonzeka kupereka nsembe mwana wake wobadwa yekha.+
11:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2017, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,8/15/1998, ptsa. 11-121/15/1987, tsa. 13