Aheberi 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:23 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 30-311/15/1987, ptsa. 13-14
23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.