Aheberi 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:29 Nsanja ya Olonda,4/15/2014, ptsa. 11-12
29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+