Aheberi 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 akukonzekeretseni ndi chilichonse chabwino kuti muchite chifuniro chake. Ndipo kudzera mwa Yesu Khristu, achite mwa ife zimene zili zokondweretsa pamaso pake.+ Kwa iye kukhale ulemerero kwamuyaya.+ Ame. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:21 Nsanja ya Olonda,12/15/1989, ptsa. 24-25
21 akukonzekeretseni ndi chilichonse chabwino kuti muchite chifuniro chake. Ndipo kudzera mwa Yesu Khristu, achite mwa ife zimene zili zokondweretsa pamaso pake.+ Kwa iye kukhale ulemerero kwamuyaya.+ Ame.