Yakobo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tikamangirira zingwe+ pakamwa pa mahatchi* kuti atimvere,+ timatha kulamuliranso matupi awo onse. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2020, tsa. 21 Nsanja ya Olonda,11/15/1997, tsa. 16