10 Koma mukavutika kwa kanthawi,+ Mulungu, yemwe amapereka kukoma mtima konse kwakukulu, amenenso anakuitanirani ku ulemerero wake wosatha+ kudzera mu mgwirizano wanu+ ndi Khristu, adzamalizitsa kukuphunzitsani. Adzakulimbitsani+ ndi kukupatsani mphamvu.+