1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:22 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, ptsa. 16-17 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 228
22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+