Yuda 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+ Yuda Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10 Nsanja ya Olonda,6/1/1998, tsa. 17
10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+