Yuda 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma inu okondedwa, kumbukirani mawu amene atumwi a Ambuye wathu Yesu Khristu ananena kalero,+