Chivumbulutso 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, ndikukulangiza kuti ugule kwa ine golide+ woyengedwa ndi moto, kuti ukhale wolemera. Ugulenso malaya akunja oyera uvale, kuti maliseche ako asaonekere+ chifukwa ungachite manyazi. Ndiponso ugule mankhwala opaka m’maso+ ako kuti uone. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:18 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 313/15/2007, tsa. 145/15/2003, tsa. 1910/1/2002, ptsa. 21-2212/15/2001, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 68-71
18 Chotero, ndikukulangiza kuti ugule kwa ine golide+ woyengedwa ndi moto, kuti ukhale wolemera. Ugulenso malaya akunja oyera uvale, kuti maliseche ako asaonekere+ chifukwa ungachite manyazi. Ndiponso ugule mankhwala opaka m’maso+ ako kuti uone.
3:18 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 313/15/2007, tsa. 145/15/2003, tsa. 1910/1/2002, ptsa. 21-2212/15/2001, tsa. 32 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 68-71