Chivumbulutso 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo mkaziyo anali ndi pakati. Iye analira pomva ululu+ chifukwa cha zowawa za pobereka. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 177-178