Chivumbulutso 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso zitseko za pazipata 12 zija zinali ngale 12. Chitseko chilichonse chinali ngale imodzi.+ Ndipo msewu waukulu wa mumzindawo unali wopangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:21 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 307-308
21 Komanso zitseko za pazipata 12 zija zinali ngale 12. Chitseko chilichonse chinali ngale imodzi.+ Ndipo msewu waukulu wa mumzindawo unali wopangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi.