Chivumbulutso 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma chilichonse chosapatulika, ndi aliyense wochita zonyansa+ ndiponso wabodza,+ sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo olembedwa mumpukutu wa moyo, umene ndi wa Mwanawankhosa.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:27 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 306, 310
27 Koma chilichonse chosapatulika, ndi aliyense wochita zonyansa+ ndiponso wabodza,+ sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo olembedwa mumpukutu wa moyo, umene ndi wa Mwanawankhosa.+