Mawu a M'munsi
“Mwezi wachiwiri” umene ukutchulidwa m’vesili unadzakhala mwezi wa 8 pakalendala yopatulika imene Yehova anapatsa Aisiraeli atatuluka m’dziko la Iguputo. Mwezi umenewu, wotchedwa Buli, unkayambira chapakati pa October n’kutha chapakati pa November. Onani Zakumapeto 13.