Mawu a M'munsi
“Mwezi wa 7” umene ukutchulidwa m’vesili unali kuyenderana ndi mwezi wa Abibu pakalendala yopatulika ya Ayuda. Pakalendala ya Ayuda imeneyi, mwezi wa Abibu kapena kuti Nisani, unali mwezi woyamba.