Mawu a M'munsi
Aheberi ankagawa usiku m’magawo atatu, ndipo uwu unali ulonda wachitatu komanso womaliza. Unali kuyamba cha m’ma 2 koloko usiku mpaka 6 koloko m’mawa.