Mawu a M'munsi “Uchi.” Zikuoneka kuti uwu si uchi wa njuchi koma ndi madzi azipatso, chifukwa ukutchedwa zipatso zoyambirira. (Le 2:12; 2Mb 31:5)