Mawu a M'munsi Kutanthauza chovala chimene nsalu yake anaiwomba mophatikiza ulusi wa thonje ndi ubweya wa nkhosa. Onani De 22:11.