Mawu a M'munsi “Kudzisautsa” pano kungatanthauze kusala chakudya ndiponso kutsatira malamulo ena ofanana ndi kuchita zimenezi.