Mawu a M'munsi Akutchedwa Mwefuraimu chifukwa anali kukhala kudera la Efuraimu, koma kwenikweni Elikana anali Mlevi. Onani 1Mb 6:19, 22-28.