Mawu a M'munsi Mawu akuti “ekala” pano akutanthauza malo amene ng’ombe ziwiri zingathe kulima tsiku limodzi.