Mawu a M'munsi
Umenewu unali mzinda wa m’dera lamapiri la Yuda, umene unali pamtunda wa makilomita 12 kum’mwera kwa Heburoni. Si wofanana ndi phiri la Karimeli. Onani Yos 15:20, 54, 55.