Mawu a M'munsi N’zotheka kuti zaka 40 zimenezi akuziwerenga kuchokera pamene Davide anadzozedwa kukhala mfumu. Onani 1Sa 16:13.